ACHITA CHANI MAYIWA? Munthawi yawulamuliro wachipani cha DPP, - TopicsExpress



          

ACHITA CHANI MAYIWA? Munthawi yawulamuliro wachipani cha DPP, kunachitika chitukuko chowoneka ndimaso monga mwazina; Parliament Building, Malawi University of Science and Technology, 5 Star Hotel, Masauko Chipembere Highway, Maize silos, Nsanje inland port ndi zina zambiri. Nanga chilowereni mboma pa 7 April, 2012, ndichani cholozeka chomwe Mayi Banda ndi chipani chawo cha PP achita? Ife a Bnm tikuti kuyika myala yamaziko ndi uchembere wabwino, nanga inu? #Linda wa #Bnm.
Posted on: Sun, 03 Nov 2013 18:37:00 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015