Adm chonde aziwitseni anthu maganizo angawa. Ndikanakondwa - TopicsExpress



          

Adm chonde aziwitseni anthu maganizo angawa. Ndikanakondwa kwambili dziko la malawi likanachita ngati zomwe lachita dziko la uruguay povomeleza ulimi komanso malonda a chamba. Kwathu kuno tili nd anthu ambili amene amachita zimenezi. Despite kuti zimabweletsa ndalama anthu mkumatukuka koma lamulo limaletsa(chamb atu chomela mnthaka). Tsono boma ndi mabungwe mmalo mopanga fight kuti chamba chivomelezedwe anthuwo atukuke mwaufulu ali busy kupanga ma kampeni ati tivomeleze maukwati a amuna kapena akazi okhaokha, pali mzelu? Kampeni ikuchitika ya maukwati a anthu ofanana ziwaloyo bwezi ili yophuzitsa maconditions a ulimi ndi malonda a chamba. Why fighting for
Posted on: Mon, 05 Aug 2013 08:56:25 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015