Bungwe la Football Association of Malawi lalembera chikalata Team - TopicsExpress



          

Bungwe la Football Association of Malawi lalembera chikalata Team ya Silver Striker ndipo ayipansa maola 48 kuti iyankhe ngati mulandu omwe awasegulira akuukana kapena ayi Muchikalatachi chikufotokoza zinthu monga izi: Team ya Silver Strikers inalephera kuletsa ochemerera awo mundime yosiriza ya chikho cha Standard Bank pomwe amsangalala atagonjetsa Team ya Azam Tigers 1-0 zomwe nzosutsana ndi malamulo ampikisanowu Ngati Silver ingavomere mlanduwu ikuyembekezereka kupereka chindaputsa cha ndalama zokwana k1.5m kamba ka kuononga zinthu zina za Bankiyi komanso zopezeka pa bwalo la Civo
Posted on: Wed, 10 Sep 2014 05:22:09 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015