Felix and Tapiwa in bed at night!.. Felix: (Adangoyamba - TopicsExpress



          

Felix and Tapiwa in bed at night!.. Felix: (Adangoyamba kuphaphasa uku akugona.Ndiye kaya amadziwa kaya samadziwa adapezeka kuti akusisita mkazi wake. Adayambira kumutu uyo pamimba uyo akutsetseleka,tiye tiye uyo wafika uku gwira gwira gwirani.Basi kenako adangosiya) Ataona izi tapiwa adafunsa mwamuna wake mkhutu-mkhutu. Tapiwa: Kodi darling mwasiyanso ndimamva bwinotu... Felix: Pepani ndidakugunda ndimafufuza remote ndiye ndaipeza.. Tapiwa: ...........??? #advisor02
Posted on: Tue, 23 Sep 2014 10:52:43 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015