Ma Admin ena a Malawi Breaking News and Gossip akukhala mwamatha - TopicsExpress



          

Ma Admin ena a Malawi Breaking News and Gossip akukhala mwamatha Prophet Wina atawawuza kuti chaka chino sachimaliza Ma admin-wa akhala akulemba kuyambila dzulo nkhani zonyoza Prophet-yu Iwo anapostamayina atsikana omwe akuti ndizibwenzi za a Major ndipo anati onse amadyedwa plain Lero prophet uja wayimva ndipo wawawuziratu kuti chaka chino sachimaliza Ma admin-wa akupepha kuti muwathandize kupephera kuti angonjetse mphamvu za prophet-yi zomwe iwo akuti ndizochokera kwa satana #Mßwèè
Posted on: Wed, 24 Jul 2013 15:39:58 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015