Mareport akusonyeza kut JOSEPHY JK SHAKIRA KAMWENDOH nthaw - TopicsExpress



          

Mareport akusonyeza kut JOSEPHY JK SHAKIRA KAMWENDOH nthaw iliyonse atha kufika mdziko muno ndikuzaseweleranso mpira ku team yake yokondedwa ya WANDERERS, izi zili chomwechi kamba kot ku mozambique panopa kwavuta sikuli bwino nde mateam akungokhala sakusewera mpira, mphunzitsi wamkulu wa team yomwe amamenya JK wati alora ma profesional onse kut abwelere kaye ku dziko lakwawo kt azabweleranso kusagwilizana kwa akuluakulu a dziko la mocambique kukazakha. Ngat angafiked katswiliyu tikuziwisani #LICKY
Posted on: Mon, 28 Oct 2013 12:19:43 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015