Tikufuna ma admin azitithandiza kulembapo nkhani pa page yi - TopicsExpress



          

Tikufuna ma admin azitithandiza kulembapo nkhani pa page yi zochitika mmadera mwanumo. Dziwani kuti ntchito yi ndiyaulere ndipo ndiyopanda salary. Ma Admin wa tikufuna akhale motere 1. Chitipa awiri 2. Karonga awiri 3. Mzuzu atatu 4. Rumphi awiri 5. Mzimba awiri 6. Nkhatabay awiri 7. Kasungu awiri 8. Nkhotakota awiri 9. Salima awiri 10. Dowa awiri 11. Ntchisi - awiri 12. Mchinji awiri 13. Dedza - awiri 14. Ntcheu - awiri 15. Lilongwe - alipo kale 16. Nsanje - awiri 17. Chikhwawa - awiri 18. Mwanza - amodzi 19. Neno - amodzi 20. Blantyre - alipo kale 21. Zomba - alipo kale 22. Balaka alipo kale 23. Mangochi awiri 24. Machinga awiri 25. Chiradzulu - alipo kale 26. Phalombe - awiri 27. Mulanje awiri 28. Thyolo - awiri 29. Likoma Dziwani kuti nukuyenera kukhala ndi MSCE, non-partisan komanso oti muli ndi phone ya internet osati odalira ya ku (bureau). Mukhalenso oti simumazalemba nkhani zonyoza anthu ena chifukwa anakulandani akazi ayi. Our page has grown to over 19, 000 likes and that shows the trust people got on this page, so any admin who will compromise that will be removed. Once you are made admin, a notification will be sent to you to inform you of that position and post, all you need to do is to go to Malawi Breaking News, Rummours, Vacancies & Scandals page and post the news. Those interested can contact Malawi Breaking News, Rummours, Vacancies & Scandals Chief Editor at gracekhonje@gmail or just inbox us your intentions or just comment here under expressing your wish ---GOOD LUCK--- https://facebook/MalawiBreakingNewsRummoursVacanciesScandals?ref=hl
Posted on: Wed, 10 Dec 2014 10:17:03 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015