YALAKWA. KU SHEAFFER Honde mdimin bise pliz, ndinali ku show ya - TopicsExpress



          

YALAKWA. KU SHEAFFER Honde mdimin bise pliz, ndinali ku show ya marverous. Am 18yr girl shw itatha ndinali mgulu la amene anatsalira potuluka, chaku gate lotuulukira kuja kumanani ndi anyamata atatu amaoneka kti anamwako. Amati sindinavale bwino mpaka wina anayamba kundikisa wina kundigwira manjawa kenako wina kumandipisa ukuku mwayi ndi azibambo ena omwe anawaopsyeza kuti andisiye moti ndikumva timaululu maka ukuku. Kodi kuppita ku show ya gospel nkulakwa? Nanga kapena akazife siife oyenera? Mwandichotsera uzimu ndithu
Posted on: Sun, 07 Jul 2013 16:45:02 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015