Admi hid ma id. ndine kamfana ka dzaka 20 ndili pa chibwenzi ndi - TopicsExpress



          

Admi hid ma id. ndine kamfana ka dzaka 20 ndili pa chibwenzi ndi mai winawake tinapezana pa fb. mai ameneyu amakhala ku mangochi amachita kubwera kno ku Bt kma amati sali pabanja kma siku lina tikufewesana ndinazapeza ring mu handbag yake kumfunsa anakana kma anthu andiuza kt ndizowona ndipo mai ameneyo ali ndi ana 4 mwana wake oyamba ali ku ABC. kma ine ndalemba mayeso a 2 kdi abale awa simaloza kapena azimayi ndimumene mulili kunama? ndithandizi ndipitilize ku menya mzimayiyu ngakhale akukoma kwambiri kapena ndisiye
Posted on: Sat, 13 Jul 2013 19:17:32 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015