Admin:ndithandizeni nkhaniyi Kuno ku south Africa mzathu - TopicsExpress



          

Admin:ndithandizeni nkhaniyi Kuno ku south Africa mzathu wasowa Sakuziwaka komwe ali,pomwe tikunena pano khongona zathu zizikungwila: Dalitso kakhuni amakhala kuno ku Heidelberg ndipo amagwira ntchito ngati mulonda ku kampani ina yotchedwa crimestop. Asowa mosadziwika bwino amuthawa mkazi komwe ali sakudziwika.amusiyira ana awiri wamamuna ndi wamkazi.moti panopa mkaziyo ndi anawo akusungidwa ndi bungwe la social worker. #chindinho
Posted on: Tue, 24 Sep 2013 10:11:10 +0000

Trending Topics




© 2015