Am sure Malawi ali mtulo..why is Peter akukhala ngati wagona? kodi - TopicsExpress



          

Am sure Malawi ali mtulo..why is Peter akukhala ngati wagona? kodi wagontha moti sakumva zomwe a Malawi akudandaula? ngati ndi choncho kodi mkazi wake alikuti osadzutsa amuna akewo? chabwino mwina ali buzy kuchengeta abambowo kuchipinda..nanga alangizi akewo akutani? mwina akudya, kaye alikuti mabungwe omenyela ufulu aja? kodi iwe Voice Mhone basi utha choncho? kodi a Chakwera mukutani? ifetu timaganiza kuti utsogoleri wanu uwoneka nyengo ino powachangamutsa a Mutharika kupanga zinthu zopulumutsa malawi pamene akumka komila..kodi mudalipo nthawi imene a Tembo amkachangamutsa a Bingu kupanga zinthu zopindulira Malawi? Tinene kuti otsutsa ndi olamula nonse ndinu zitsilu simukudziwa chochita? mthawi ino ndiyanu a Chakwera kuti dziko lidziwe kuti kuli otsutsa othandiza ngati mmene amkachitira bambo Tembo..sinthawi yokhala pansi ino kapena kumangokhala chigawo chapakati..yendani ponse kumpoto kaya kummwera tidziwe kuti ndinu munthu olabadira anthu anu..kapena akuikani chimanga chophika mkamwa? Changamukani..!!.
Posted on: Mon, 08 Dec 2014 22:49:04 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015