Anyamata ena omwe mayina awo sititchula koma ndi Amalawi amenyana - TopicsExpress



          

Anyamata ena omwe mayina awo sititchula koma ndi Amalawi amenyana kwambiri polimbira nkazi wachikaladi ku Bevell Nkhani ikuti mnyamata mmodziyo amagwira ntchito ya u driver kwawo kwa ntsikanayo ndipo anapanga chibwezi ndi mwana wabwana wakeyo tsono tsiku lina anamutenga nzakeyo kuntchitoko ndipo ntsikana uja anadyereraso maso wa mamuna winayi mpaka kupatsana ma no ndipo akhala akududuluzana mozembera winayi tsono dzulo tsiku la 50 linakwana pomwe bwezi lake anapezerera ntsikanayi kumnyumba kwa nzakeyi ndipo ndewu inabuka mpaka wina wavulala kwambiri Langizo Chonde anyamata pangani zomwe munabwerera musatichititse manyazi #linly
Posted on: Wed, 26 Nov 2014 18:17:18 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015