Bengo ku Trip Ya Ku Egypt Aphunzitsi ndi ana onse limodzi - TopicsExpress



          

Bengo ku Trip Ya Ku Egypt Aphunzitsi ndi ana onse limodzi bengo adali pa u lendo wa ku egypt,kukaona zithu zosiyanasiyana muja zikhalira inu...ali mu njira aphuzitsi adafunsa.kodi ana inu president wa ku egypt ndi ndani mmm iwe Bengo? Bengo: I dnt know madam Teacher. : y? You must focus on your study Bengo: madam may I ask u question? Tchr: yes go a head Bengo: do u know mary , do u know rose Tcher: no Bengo: wat about Linda ? Tchr: y u ask me pipo who I dnt know? Bengo: yae from today u must focus on your husband Tchr: (end up no answer) Ulendo unapitilira ndipo anafika pa manda a Farao .Ndipo panalembedwa kuti 1398BC Teacher: kodi ana inu number imeneyi ikutanthauza chani? Ana onse anali ziiii .only Bengo yekha anaimika zanja Aphunzitsi anakhala ngati sakumuona komabe panalibenso wina anayimika nkono Teacher:(monyinyilika)mmm Bengo Bengo(with confidence) madam imeneyi ndi BBM pin ya Farao One word for me +27711963965 293BB2C4
Posted on: Tue, 08 Jul 2014 18:36:00 +0000

Trending Topics



#162 Female From Chaamu :p admin 5 baar send kr chuki hu abki
O que precisamos para aprender a jogar é termos um pouco de
TAX AUDIT APPLICABLE TO PARTNERS ON INCOME FROM PARTNERSHIP
A state-wide polio vaccination that targets children from birth to
In todays world, we have bored husbands and tired wives. For men,
Wow so on weekend i basically wrote a status up and damn brothers

Recently Viewed Topics




© 2015