Coach wa team ya Bullets Eliya kananji wapempha wosatira - TopicsExpress



          

Coach wa team ya Bullets Eliya kananji wapempha wosatira bullets wonse kuti adekhe ndikuwapasa pata anyamata asopano Jafalie Nan Chande,Davie Ngambi ndi Frazer Menyani!!! Kananji wati masapota asayembekezere Miracle kuchoka kwa akaswiriwa kamba kakuti iwo ali ngati palyer wina aliyese!! Mau ake Sir Kananji wati wosatira abullets asadere khawa kwambiri ndi mene team yamenyera dzuro !! Ndikakamba nawo anyamata lachiwiri zakuyipa koderera team, chomwe chikufunika ndi 3points pagame yili yonse kuti Timuyi itenge league!!
Posted on: Mon, 08 Sep 2014 04:37:56 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015