Coach wa team ya fuko Sir Eliya kananji wati iye sakuonapo - TopicsExpress



          

Coach wa team ya fuko Sir Eliya kananji wati iye sakuonapo cholepheretsa kutenga league czon yino ngakhale palipikisano ndi moyale!! Kananji wati bullets yikumenya bwino koma kungoti ma team ambiri akumakozeka kwambiri akamakumana ndi team yafuko!! Iye wati wosati bullets asade khawa!! Paza Frazer hitman menyani Sir kananji ati mwanayi ndiwovulala komano game ya wAnderers azakhala ali fit!!! Enjoy your day!!! Sms BB ku 1515!! Mr jabu!!!
Posted on: Mon, 15 Sep 2014 06:55:00 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015