Copied from "Paparazzi Pa Malawi page" Mnyamata wina wodziwika mu - TopicsExpress



          

Copied from "Paparazzi Pa Malawi page" Mnyamata wina wodziwika mu town ya Blantyre amene amakonda kupanga program ya Kids buds pa MBC/TV matsiku ambuyomo, ali wachichepere, anasintha maso mphenya ake, pano ndikaswiri ogulitsa mankhwala othandiza anthu ku bed, mnyamatayu amene ma customer ake ambiri ndi ma vendor, amayenda ndi ma pills nthawi ina iliyonse, malingana ndi kafukufuku wathu ma vendor ambiri akumusimba kwambiri mu town ya Blantyre and Limbe,,,,,"Belita akuwa utsiku walero, atero vendor wina ogulitsa msapato ku Blantyre"
Posted on: Thu, 04 Jul 2013 16:47:41 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015