DRIVER WINA ANAGUNDA ANTHU 25 NDIKUPHERATU POMPO, TRAFFIC POLICE - TopicsExpress



          

DRIVER WINA ANAGUNDA ANTHU 25 NDIKUPHERATU POMPO, TRAFFIC POLICE INAMUPEZA. POLICE: iwe driver zinakhala bwanji kuti uphe anthu onsewa? DRIVER: ineyo ndimathamanga kwambiri zedi, ndikuti ndizipita chakumazereku mwadzidzidzi ndinaona anthu ambiri, koma kumazereku kunali munthu mmodzi, basitu zinachitika. kukhala inu mungati? POLICE: unakakhotera kumazere ugunde mmodziyo ambiri apulumuke. DRIVER: ndizimene ndinachita, ndinasiya anthu ambiriyo kuti ndigunde iyeyo. uchitsilu wake iyeyo anathawira kumene kunali anthu ambiriko, amaona ngati sindinamuone ndinamutsatabe konko mpaka waphetsa amzakewo!!
Posted on: Sat, 02 Nov 2013 09:01:00 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015