DZUKA MALAWI! mayi wina wake wa chizungu anapita ku beach - TopicsExpress



          

DZUKA MALAWI! mayi wina wake wa chizungu anapita ku beach kokasangalala mmadziwa October ku tentha. Anavala dress yokha nothing in side ndiye mphepo ikaomba mayi uja samalabadira kugwirira dress ija ayi koma amagwirira kwambiri chipewa chake. Thabo anamfusa mzimayi uja kuti mukutionetsa akatundu amayi bisani, mayi uja amvekere what you see down there is 50years old,and my chipewa is brand new and expensive
Posted on: Sat, 30 Aug 2014 07:50:19 +0000

Recently Viewed Topics




© 2015