Evening to you all... Job interview. . Kampaní - TopicsExpress



          

Evening to you all... Job interview. . Kampaní ina inalengeza kuti ikufuna driver wa truck ndipo Akhale ndi certificate ya std 8..komanso Akhale oti wapitako kunja..pokumva izi man ena anaona kuti mwayi wapezeka ndipo anavaya komko..zinali chonchi. Bwana: ndikhulupilira uthenga mwaumva. Man: eeeh. Ndaumva. Bwana: moti ku South Africa mwakhalako?? Man: kwambili. .zaka zitatu. Bwana: ku Zimbabwe mwayenda?? Man: kumeneko nde zaka 5. Bwana: nanga ku Botswana? ? Man:kumeneko zaka zitatu. . Bwana:nanga ku Zambia? ? Man:kumeneko nde ndinatchona komko moti apa ndikuchokela komko. . Bwana:zosangala tsa kwambili. .apa nde kuti Geography mukuyidziwa. Man: kumeneko ndakhalako zaka 8. Bwana: kutiko mwakhalako zaka 8ko. Man: ku Geographyko..nd imakhala pa Shop paja..
Posted on: Fri, 28 Nov 2014 18:48:44 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015