GUYS KODI NDALAKWITSA KUMUUZA JANE CHILUNGAMO?! Ndinaponya ka - TopicsExpress



          

GUYS KODI NDALAKWITSA KUMUUZA JANE CHILUNGAMO?! Ndinaponya ka post pompa kuti ndikufuna mkazi opilira ndithu chifukwa chida changa chokodzera ndilibe anandichotsa ku chipatala. Nde Jane anandishosha ku inbox-ku kufuna kudziwitsitsa mpaka macheza anafika pokoma ,mpaka zinafika popatsana ma fone numbers. JANE:.. Tandiuza chinachitika mchiyani kuti ukuchotse chida chako?! Tsono poona mwayi sindinafune kunama ndinafuna kunena zoona zake zenizeni za zimene zinachitika kuti achipatala akafike pochotsa chida-cho. After nditamupatsa ma fone nambala anga onse 20, anaona ngati ndine wakuba. JANE:.. Aaah iwe suli serious mpaka manambala osewo?! Ndiwe wakubatu iwe! koma.ndinamufotokozera kuti PKs:.. Munthune ndili ndi angongole ambiri nde ndimafuna asandipeze. nde Jane anamvetsetsa. Kenako ndinayamba kumuuza za zimene zinachitika kuti ndikadulitse katundu wanga ku chipatala. Ndinamuuza kuti PKs:.. Pamene ndinali boh boh ndimkazemberana ndi mkazi wa mwini, wa msilikali wina wa ku Lilongwe. Nde anandipeza tsiku lina mwini mkaziyo ndipo anandiuza kuti sandimenya koma ndingovula ndiike chida changa pa tebulo koma chosadziwa maganizo amsilikali-yo . Ndinangoona akuvala jombo yake ya nyuwani ndikukwera pa tebulo ndinaika katundu wangapo. Ndipo anaponda chidacho, ine ndinangozindikira ndili ku chipatala ndipo adotolo ndi omwe adandiuza kuti mwini mkaziyo ndi amene adanyenya malipyata angawo ndi jombo yake ya nyuwani ija. Nde panalibe njira ina koma kungochotsa chida chonyenyekacho.... Ndiye eti abale mkazi ndamuuza zimenezi dzulo usiku sanandiyankhe chilichose., mmawa wa lero ndapeza wandibloka. Ndinalakwa kumuuza chilungamo abale? PKs...
Posted on: Wed, 06 Aug 2014 09:06:33 +0000

Trending Topics



0px;">
Killer Filter Replacement for REICHDRILL 5PS5304-1 CK1H9BI Killer
Interested in learning techniques to develop increased finesse

Recently Viewed Topics




© 2015