GUZANI NDI MWANA WAKE LAMBULANI "Dad...ine ndi a anzanga ku - TopicsExpress



          

GUZANI NDI MWANA WAKE LAMBULANI "Dad...ine ndi a anzanga ku School timatsutsana....wina amati anafe mumachita kutigula ku chipatala....ena amati mumachita kukatiwedza ku nyanja kodi eti ndi zoona?". Anatelo mwana Lambulani mwana wa Guzani pofusa bambo ake. "Ana...ife makolo timachita kugula kuchipatala....ena ndi zoona timachita kuwedza mu nyanja" Anatelo naye Guzani poyankha mwana wake. "Dad...nde ngati mumachita kutigula bwanji kwa ALEKENI kuja kuli ana 10....koma banja limene lija ndilosauka...kodi angakwanitse kugula ana onse aja" Anafusanso Lambulani. "Kumene kuja a LEKENI amachita kutenga pa ngongole ana ena" Anatelonso Guzani poyankha. "Dad...nde ngati ana ena mumachita kuwedza mu mnyanja ya Malawi...ndekuti nyanja akalanda a dziko la TANZANIA kuno ku Malawi sikudzakhalaso ana eti?".......IPITILILA MAWA!!!!
Posted on: Sun, 25 Aug 2013 17:29:26 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015