Guyz allow me tu thanx diz pipo:MR AMIN{Sir mumasiya zintchito - TopicsExpress



          

Guyz allow me tu thanx diz pipo:MR AMIN{Sir mumasiya zintchito zanu kuzathandiza anyamata ku ground Mulungu abwezeretse zimene mumalephera kukumana (kupeza) nazo chifukwa cha kumpira, timakunyadirani ife},MR CHAPWETEKA{Sir timathokonza chifukwa chakuzipeleka kwanu mumasiya zanu zintchito wa ku ground Mulungu apitilize kukuonjezera mphamvu ndi lutha, Timakunyadirani nanunso},MR HENZ{mumathawa kuntchito ulendo waku ground konseko kufuna kutchukitsa Nsanama pankhani ya mpira timathokonza pazimenezi Abwana mumapanga, Mulungu apitilize kuyendetsa bwino ntchito yanu,Muli sharp},PLUS THIZ GUYZ:Lucas,Chief Kondoni,Gelie man,Lovemore,Ernest,Charlie,Victo,Thilika,Rooney,Davie,Kulimyemya,Chidina,Ndi onse amene amasewera mu {NSANAMA YOUTH FOOTBALL CLUB} pamodzi ndi ma supporter onseeeee.Tipemphe Allah Apitize kutsogolera timuyi.
Posted on: Mon, 29 Jul 2013 20:10:26 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015