Hide my Id. Ndine V Kumwenda koma kwathu ndiku Dedza. Ndili - TopicsExpress



          

Hide my Id. Ndine V Kumwenda koma kwathu ndiku Dedza. Ndili pachibwenzi ndi mkazi wanga koma amakhala ku Zambia koma sitinawonane face to face. Nthawi zambiri timangocheza pa USB mwina madzuloso sometimes. Ndiye last week ya week yomwe yangothayi anandiuza kuti akufuna kubwera ndimutumizire 10 thousang kwacha, ndinatumiza 7 thousang kwacha chifukwa ndiyomwe ndinapeza. Ndiye amati abwera dzulo all the way from kitwe koma ndadikilira dzulo lonse pa petroda sanabwere. Kutumiza email direct ku yahoo sakuyankha. Kodi nditani?
Posted on: Sat, 02 Nov 2013 07:14:40 +0000

Trending Topics



t weekend is gonna be hot...!!! Friday 5/9 -- Mystique --
Josh hartnett s in penny dreadful?!? Mind....BLOWN!!!!!!!!!! And
/div>

Recently Viewed Topics




© 2015