I do not understand this? Nchifukwa chani anthu tikungoona - TopicsExpress



          

I do not understand this? Nchifukwa chani anthu tikungoona kulakwitsa kwa Kabwira instead of kuonanso kulakwitsa kwa BEAM trust and Muhlakho? To say the fact, BEAM & MUHLAKHO are devils than Kabwira! 1. Ndalama zomwe anatenga ku NAC zikanagula ma ARV angati (akanati agule ma ARV). 2. Ma ARVwo akanapulumutsa miyoyo ingati? 3. Ndi anthu angati amene ali ndi HIV amene angapange survive without ARVs? Now, wina watenga ndalama zoti zikanatha kugulila ma ARV nkukapangila ma workshop, kugulila ma bin komanso kugawana ngati ma allowance. Wina wadzuzula zonyasazi... Ali bwino ndi uti? Lero aMalawi tikuti oyipa ndi amene wadzudzulayu. Wina mpakana kupanga ka press conference akuti Kabwira apange resign. REALLY????????
Posted on: Thu, 18 Dec 2014 06:53:22 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015