I feel pity wth Vuwa Kaunda.Nthawi ya Bingu anthu tikufuna - TopicsExpress



          

I feel pity wth Vuwa Kaunda.Nthawi ya Bingu anthu tikufuna kuwamatcha a Vuwa adali busy kuzungulira dziko la Malawi komanso pa TV kuwuza anthu kuti adzapite ku statehouse ku Lecturing osati kumsewu koma pamapeto pake anthu adapita ku msewu ndipo a Vuwa Kaunda adali victim wa zionetserozo monga Malo awo a bussiness ku Biwi Triangle adaonongedwa.Lero a Vuwa Kaunda omwewo munthawi ya Peter ali busy kumawuza anthu kuti asachite Support Federism koma chifukwa cha ndalama zimene anthu akuwapatsa akuyakhula koma mumtima kodi ndizimene ziliri? Nanga zitati zathekadi a Vuwa Kaunda mpoto idzawalandira bwanji? kodi sadzakhalanso victim? Kapena angofuna kudya thumbalo koma iwonso ali mkati mochita support Federism? Zoona zake zidziwika lets wait and c.Ndangodutsamo sindidathyole nkhwani.
Posted on: Thu, 11 Sep 2014 06:02:19 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015