IZEKI NDI JAKOBO Ku Malawi kuno mpovuta kuiwala Izeki ndi - TopicsExpress



          

IZEKI NDI JAKOBO Ku Malawi kuno mpovuta kuiwala Izeki ndi Jakobo pankhani yanthabwala , komanso ma dramma Du Chisiza Junior ........,......... Chimodzimodzi England isanabwenzeretse William Shakespeare mpakana lero; wolemba mabuku uja. Munthu anamwalira pa 23rd April , 1616 : Koma palibe akumposa , anthu kumangokopera Lero ndionera Izeki ndi Jakobo mpakana tchwelofu usiku motere : 1. Padepoti 2. Alonda 3. Amu ze rodi yu woko 4. Yonamizira maliro 5. Yochekera wansembe palilaka 6. Yoweta nkhumba 7. Atelara 8 .Yangongole 9. Mntengo ku sitediyamu 10. Ulendo waku Dallas {America } 11 .Yobwerekana bokosi lamaliro 12.Njinga Osamangoti kuli Mr Bean , Clint the Drunk , Charlie Chaplain , Basketmouth , Shucks Shabalala . Zacizungu ! pena chikupitepo koma umangosekabe or sunamve nkomwe............,.............
Posted on: Thu, 25 Sep 2014 11:49:07 +0000

Trending Topics



Reduce Software Rework by Redge
For sale Honda EF 1.4 81k 2 previous lady owners! The
Here is the latest update.... On Wednesday, November 19th, I will
Una mañana un joven recibió una llamada de su ex novia en la
** Non_FarmPayrolls** ***Dollar pada perdagangan kemarin kembali
African scramble Page 27 of the history of modern world. Thus,

Recently Viewed Topics




© 2015