Iyi ndi kalata yomwe amalume ake a David a mulembela madona: - TopicsExpress



          

Iyi ndi kalata yomwe amalume ake a David a mulembela madona: Dear Madona, Thanx for adopting David Banda. Can U also come & adopt his sister Joyce Banda? akungoba zinthu za anthu kuno komanso akungoyendayend a & we are afraid, she will go missing. Mukachedwa atenga mimba kapena kumangidwa kumene chifukwa zikumveka kuti waba ndalama zambiri za anthu mmudzi muno moti amfumu akumusakasaka. Please Madona reply as soon as possible. Thanks
Posted on: Thu, 24 Oct 2013 09:27:34 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015