James Sangala wabwera poyera ndikuuza mtundu wa a Malawi kuti - TopicsExpress



          

James Sangala wabwera poyera ndikuuza mtundu wa a Malawi kuti Silver Strikers isadzivutitse kuti imutenge iye kamba kakuti mpira wa kuno kwathu adathana nawo ndipo palibe kusintha maganizo. Iye wati adzasiya mpira akadzaona tsogolo la Flames,ngati Malawi idzapite ku Brazil,iye adzakasiila kumeneko koma ngati siipita,iye apachika zipangizo zake kuti mpira wathana nawo. Koma wapampando wa Silver Strikers Dr Mafuta Mwale ati Sangala ndi munthu ndipo ali ndi chikhulupiliro chonse kuti asintha maganizo ake ndikupita ku area 47........@Andy!!!
Posted on: Mon, 22 Jul 2013 07:03:33 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015