Kafukufuku amene ndapanga akuonetsa kuti anthu ambiri amene - TopicsExpress



          

Kafukufuku amene ndapanga akuonetsa kuti anthu ambiri amene amapezeka pa facebook alibe chochita, amai ambili amalephera kugwira bwino ntchito zapakhomo chifukwa cha fb komanso salandila bwino azimuna ao akamafika kuchokera ku ganyu--bizinesi--kuntchito, chifukwa choti ati amaopa kusokoneza page,komano ma page amene amakonda ndi monga awa! zachikondi....Zakusimba....Zithunzi zolaura...Osabisirana za simba. Ma page onse alibe nao ntchito.Ndaonanso kuti izi zikuchetsa chikondi chimene mkazi amayenera kuonetsa kwa mamuna wake.Ndaonanso kuti akazi ambili amagona kapena kuti amabwera mochedwa kudzatsangalatsa njonda yao, kafukufuku akuonetsa kuti amakonda kwambili fb than thier spous, Amakhalanso aukali ana akamasewera pafupi ndiwo ati amasokoneza malyolyolyo apa facebook.Its not bad to be at facebook but lets not forget our mission.
Posted on: Mon, 14 Oct 2013 09:50:22 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015