MCP PRESIDENT DR. CHAKWERA IS A PHARISEE, AN EMPTY TIN THAT MAKE A - TopicsExpress



          

MCP PRESIDENT DR. CHAKWERA IS A PHARISEE, AN EMPTY TIN THAT MAKE A LOT OF NOISE - KONDWANI NANKHUMWA, MINISTER OF INFORMATION Bambo Kondwani Nankhumwa omwe ndi Nduna ya za nkhani awanena Dr. Chakwera omwe ndi President wa MCP kuti ndi mfalisi [A falisi ndi anthu aja amanenedwa ndi Yesu kuti amanamizila kupanga zinthu ngati angelo koma zili zinkhalambo] A Chakwera asamapangitse ma Press conference kumanyoza boma ngati kuti iwowo angakwanitse kuyendetsa iyayi. Boma siphadatu. Boma si church yi. Ngati amakwanitsa kuyendetsa kampingo asawone ngati angakwanitse kuyendetsa boma yi, a Nankhumwa adalankhula motero As far as [DPP) Government is concerned, there will be no empty theatrical gestures or actions or pronouncements, no prancing on the stage and no flagellation, but we will simply continue to act against the suffering of our people, as decisively as we have sought and resolved to, without being seduced to do otherwise by holier than thou sentiments of those that are obsessed with the desperation of seeking cheap political capital from the sanctuaries where the untried and the untested hide, who because they are in the safety of not being in office, and who by possessing the advantage of not being on the stage of public scrutiny, pretend to be present day Messiahs with all the answers. adawonjezera mu chizungu cha mabomba
Posted on: Wed, 10 Dec 2014 05:44:33 +0000

Trending Topics



stbody" style="min-height:30px;">
MUMS! does your child suffer with any of the following?
So as I have my awkward yard sale on a Wednesday, I sit out there
Black Friday and Cyber Monday Deals Buoy Rod Only 1/2 X

Recently Viewed Topics




© 2015