Munthu watha mau uyu eish Ruth Jere Amene muli joni - TopicsExpress



          

Munthu watha mau uyu eish Ruth Jere Amene muli joni osamatitenga ifeyo tili ku malawi kuno ngati opusa, mukumapanga update tima status tanu topusa kumati am going out for week end, I have birthday part,on my way to the beach, ndizina zotelo chosecho mungonama mukupita kokaola manyi agalu ndi kukatchtcha kapinga, akazinu mukupita kokasuka zimbuzi za azungu ndi kukalera ana azungu, timanyumba tanuso tomwe mukukhala mulibe malo osambira komanso toilet,pomwe ifeyo kuno tikusangalala kuposa inuyo akapolo inu.tamangobwera basi iyaaa!
Posted on: Mon, 14 Oct 2013 12:43:34 +0000

Recently Viewed Topics




© 2015