Mzina lamulungu mwini chifundo. Mwini chisoni chosatha all allah.. - TopicsExpress



          

Mzina lamulungu mwini chifundo. Mwini chisoni chosatha all allah.. ndikuthokoza pondiposa moyo wautali kufikira lero pa 07/1/2015 ndikupepha ndisomgolelenibe monga mwa zaka zonse. all allah popanda inu ndine yana?..(without allah lm nuthing)..kuchokera mchaka cha1986 ndinabadwa mayi & bambo ali osangalala ndi chimwe uku kunali ku CHIPATALA cha NTCHEU BOMA in MALAWI. Mayi ndikuphepha allah akusogolene moyo wautali pondisamalira moyo wangau pamodzi ndi bambo asalamu allikum
Posted on: Wed, 07 Jan 2015 12:46:44 +0000

Trending Topics



a wedding
I know that the post I shared about the colony that was poisoned
Cyber Monday MY MINI GOLF SCHOOL TEAM SET Rating: 5 out of 5

Recently Viewed Topics




© 2015