Pamene team yikukozekera kupita ku Lilongwe,Training ndiye - TopicsExpress



          

Pamene team yikukozekera kupita ku Lilongwe,Training ndiye yayambapo ndipo anyamata onse alipo kupatula akatakwe awa omwe ali mu squad ya flames!! Mkango Plus Sakhani!! Mussa Manyenje!! Bashil Maunde!! Vin Gona!! Mussa Manyenje!! Ndi Victor Vibre Limbani!! Pakali pano tili ndi player wasopano koma anali ku team yathu kalero!! Raqib Milanzie!! Zambiri mumva kwa #frazer!! Mazuro pano!! Mr Jabu!!!!!
Posted on: Tue, 23 Sep 2014 11:11:40 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015