Press Release: Pofuna kusangalatsa thupi lake, kusaka makobili - TopicsExpress



          

Press Release: Pofuna kusangalatsa thupi lake, kusaka makobili komanso kucheza ndi anzake tsiku la lero monga friday, Greyson Chapita ayenda chonchi: 8am- Wellcome Trust ku ntchito. 9:30am - Limbe kwa amwenye kukawaponda makoboli. 11am - Ku bank kosunzumila salary ngati yalowa 11:45am - Kotunga madzi ku queens. 12pm - Kotenga mwana ku sukulu 2pm - Kuntchito 4pm - Ku Kaya Lounge macheza kuyambikapo 6pm - Kotunga madzi 8pm - Mount soche sportsmans bar kowonela mpira ndikudya sheen. 11pm - Blue Elephant 1am tsiku linalo- Chez Mutha kundipeza kulikonseko poyimba nambala yanga ija muli nayo ija #Management
Posted on: Fri, 23 Jan 2015 04:53:51 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015