Signs that the man you are dating azakusungani - TopicsExpress



          

Signs that the man you are dating azakusungani akazakukwatirani 1. Akayimba phone ndikumaliza samapanga check balance, ngati amapanga check dziwani muzakhala pamavuto owopsa 2. Ngati ali ndi laptop, operating system yake ndi chani? Ngati ili XP dziwani kuti muli mmadzi 3. How often he buys new underwear. Nanga mwamuna kumatha chaka asanagule pant wanyowani eeeish 4. Kumanama kuti safuna mkazi okudya pizza ati zimanenepesa. Bodza ili akakuzunzani ndi khwanya 5. Ngati amakagula nsapato zovala mu Bata, thawani azizakuvalikani sofia 6. Chiyambireni chibwenzi sanakutengeniko kupita pamalo ena ake 7. Nyimbo zimene amakonda. Ngati amakonda ma blacks, ndi wachamba. Ngati amakonda gospel kwambiri ndi virgin kapena wamanyazi, ngati amamvera mbenjere ndi trad. Thawani. 8. How he treats his sisters will tell you whether you are self or not 9. Chimwamuna monse chayambira my mom this, my mom that, uyutu azizapanga za masiteni ake osati za iwe ndiye samalani 10. Mwamuna wa nsanje ukavala zowonetsa bere kapena dinda azidandaula kukuwuza kuti sunavale bwino. Azakusunga ameneyu #Linda
Posted on: Tue, 19 Nov 2013 05:55:39 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015