The road to morroco Ma player a silver strikers amene adzamenye - TopicsExpress



          

The road to morroco Ma player a silver strikers amene adzamenye nawo game ya saturday Lucky malata ( vice captain) Combination ya Harry nyirenda ndi Malata ndi imene ipitilize ntchito yotseka kumbuyo loweruka lino mothandizana ndi FM7 komanso Mzava kapena kintu Lanjesi Zatsimikizikanso kuti James shareholder sangala sapatsidwa mwai okankha chikopa pa masewera amenewa DR Frank Faza Banda Faza ali ndi mwai waukulu osewera loweruka lino ndipo sizochita kufunsa. Faza ali ndi mwai waukulu chifukwa amatha kusewera kumanzere mmbali( left wing) kusewera ngati attacking mildfielder, kusewera ngati defending mildfielder komanso ngati false number 10. Chifukwanso chakuti ali ndi Luso lomwetsa zigoli zomwe ndi zimene flames ikufuna,khulupilirani,mumuona faza akukankha chikopa loweruka lino Young ju chimodzi (injured) Pano mwai wa ju woti amenyenso ku national team watsekerezedwa atavulala ku training . Ju akuyembekezereka kukhala osasewera mpira kwa two weeks. Aka sikoyamba kuti mwai wa Ju usokonekere chonchi. Pa game ya Benin,ju anachotsedwa pa 18 man squad pa 11th hour chifukwa cha malungo. Injury ya Ju ikusonyeza kuti asemphana ndi return leg ya Algeria unless e miracle happens Meanwhile a supersport atsimikiza kuti game ya malawi ndi algeria idzakhala LIVE pa supersport 4. Tibwererezenso kuti continent yonse ya africa idzakhala ndi mwai owona amalawi akukangantha algeria via supersport 4. Zabwino zonse ma flames Bring on algeria Moto kuti buuuuuuu
Posted on: Thu, 09 Oct 2014 04:40:08 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015