Ya manyadzi idafera ku una guys Ndine mzimayi wachichepere - TopicsExpress



          

Ya manyadzi idafera ku una guys Ndine mzimayi wachichepere ndimakhala ku crester munthu ine poyamba ndimagwira bwino nchito then ndinazavaya ku malawi according holiday inakomesesa ndinadusa matsiku ndimachengeta anyamata apa malawi kaye nditafika kuno bwana wanga wandiuza xoti nchito yatha kamba koti ndakhalisa ndiye pano ndikusaka ntchito omwe averako antha kundiimbira pa 0782014136 #Rose_Ndhlovu ngati wina aliso ndi malo okhala atha kundiimbira bcz pano zithu sizili bwino zikomo #Sharp
Posted on: Tue, 30 Dec 2014 09:07:55 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015