ndine mtsikana wa zaka 17.ndangomaliza kumene mayeso anga a MSCE - TopicsExpress



          

ndine mtsikana wa zaka 17.ndangomaliza kumene mayeso anga a MSCE ndimaphunzira pa New era.ndimakhala ku Katoto,mzuzu.eti dzulo aphuzitsi anga amuna kunditenqa pa galimoto yawo akuti akandisiye kunyumba..nde ine ndinalola potiso transport ndinalibe..ndeno tafika Ku Lilongwe ndi usiku nde tinapita ku Kalikuti hotel tadya then anandikakamiza kuti tigone limodzi ku roomz.[munali ma bed awiri koma ndagona ndiwowo].eti abambowa kumandinyengerera ati angolawa ndawasangalatsa, andichitira zazikulu .ndinachita manyazi poti anandithandiza transport ndinalibe..mpakana ine ndagonana nawo mpaka kwacha.nde ineyo ndikuopa mwina andipatsa mimba kapena matenda.ndikati chani kwathu..ine ndikuopa makolo anga amaziwa kuti ndinali ku xul osati bar..nditani apa thandizeni anzanga.musandi weruze.
Posted on: Fri, 12 Jul 2013 04:31:49 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015