Alot of dis gals wanna impress mi,koma ineyo ndimafila grace chi*2 - TopicsExpress



          

Alot of dis gals wanna impress mi,koma ineyo ndimafila grace chi*2 Eti gra,ndangomva zoti agogo ako ndi a T.A,ndangomvanso mbiri yoti ndiwe ka B.A,ukuti udzandilola mkazasiya beer,aaa iwe gra zausiru,vuto lake umamvera ma yoh!,ma yoh! ambiri ndi a nsanje ati ndilibe umunthu mmamwa monday mpaka sunday,udzinditenga ku mgonero ndikakhala ndi matsire,ndine okuda koma ndikhoza kuyera mtima fukwa cha iwe! *Singing* dis song jus meks mi laugh kkkk!
Posted on: Fri, 03 Oct 2014 01:00:13 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015