Chidzulo chabwino kwa nonse okonda masewero ampira,monga tonse - TopicsExpress



          

Chidzulo chabwino kwa nonse okonda masewero ampira,monga tonse tikudziwa kuti mawa kuli masewero aakulu ku Mangalande pakati pa ARSENAL komanso MANCHESTER UNITED apa pali masewero omwe anamenyedwapo mmbuyomu pakati pa matimuwa: /February 25th 2001----Ft Man Utd 6-1 Arsenal /November 25th 2001-----Ft Arsenal 3-1 Man Utd /October 24 2004-----Ft Man Utd 2-0 Arsenal /May 1 2011----Ft Arsenal 1-0 Man Utd. Apa pali list ya osewera a Manchester United omwe ndi ovulala: •Angel Di Maria •Daley Blind--knee •Michael Carrick--groin/pelvis •Marcos Rojo •Ashley young •Jesse Lingaard--knee •Rafael--muscular •Phil Jones--Shin •Radamel Falcao--shin •Johnny Evans--Ankle/foot Mukuganiza kuti mpirawu uzatha bwanji?Yanu ndiyiti apa kapena kuti muzaganyula yiti apapa? ****** .......#Vinjeru
Posted on: Fri, 21 Nov 2014 15:34:23 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015