FRIDAY JUMBE WANDIKWIYITSA KWAMBIRI. ATHETSA CHIPANI NGATI COMPANY - TopicsExpress



          

FRIDAY JUMBE WANDIKWIYITSA KWAMBIRI. ATHETSA CHIPANI NGATI COMPANY YAKE BWANJI? - SAM MPASU Bambo Sam Mpasu anena kuti zomwe adachita a Friday Jumbe kuthetsa chipani cha New Labour Party posapanga consult zawakwiyitsa kwambiri. Inu chipani sitithetsa ngati company yi. even company pamakhala ma procedures osati kungothetsa iyayi. adandaula a Sam Mpasu A Jumbe anati athetsa chipani cha NLP kamba koti DPP ikupanga implement what they wanted to do so no need to have the party
Posted on: Sun, 14 Sep 2014 07:29:22 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015