Good morning!! Good news is that, on sunday fomo will be leaving - TopicsExpress



          

Good morning!! Good news is that, on sunday fomo will be leaving to mozambique to play football. Masapota athu tikukupemphani kuti mulipire k500 aliyense ndipo mulandira lisiti lodindidwa fomo. Izi zayambika lero ndipo tikufuna anthu okwana 20 basi.izi zili chonchi malingana ndi capacity ya galimoto.thamangani muzalipire.mutha kubwera ku ofesi kwathu kwa nkhonya,pa ground ya mulanje secondary school nthawi ya 3pm, or mutha kutiuza pa page pathupa titha kuona kuti tikupezani bwanji.mukalipira ndiye kuti muli ololedwa kupita nafe ku mozambiki komanso .kandalamaka kathandiza kutukula club yathu. Zikomo chifukwa cha thandizo lanu. Ambuye akudalitseni.
Posted on: Thu, 17 Apr 2014 07:58:28 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015