IYI NDI MISALA MUST REED BENGO NDI NGOZO AFTER GAME YA FLAMES - TopicsExpress



          

IYI NDI MISALA MUST REED BENGO NDI NGOZO AFTER GAME YA FLAMES NDI BENIN Itatha game ya flames Bengo anakwera Galimoto ya friend ake wa kubawazi ukunso Ngozo yake ija yokonda wotchipa ija anali pakachaso. Woyamba kunyamuka anali Ngozo. Zandizandi ulendo unayambika wautali and ali munjira anangodabwa Galimoto yaima, iye ali aaaa mwina ndi ondidziwa andiimira nthawi yomweyo kukwera kutsogolo. Ulendo unayambika koma chifukwa chobawika kwambiri panalibe chomwe amayada. Atafika pokhota NGOZO anangoona chimkono chatulukira pa window chagwira chiongolero. Mantha anamugwira kenako anayangana mgalimotomo and anaona kut alimo yekha iye shaaa uwu ndiye waku Simongolia basi, atafika pa roundabout anaonanso chimkono chomwechija chatulukiranso chakhotesanso chiongolero Galimoto mkulunjika kunyumba kwa Bengo, nthawi yomweyo NGOZO ali apa pasavute mkuluphira pawindow waliyatsa liwiro wa Mbara kuti mwina kumuchere ali mmenemo kumvera nyimbo, ali mkati mosaundika wayambapo nkhani mkumawaunza anthu mbala muja amvekere ife ndi madolo moti afiti andikanika onditengatenga pano Galimoto lopanda Driver koma mkono umangolowa ikafika pokhota mkukhotetsa lapita kukamtenga BENGO, Nthawi yomweyo Bengo mkudzatulukira Mbara muja ali ndi maguy awiri, apa Ngozo mkubwebwetuka amvekere ndimati Chani!!! Ife ndi Madolo uyoo BENGO amukanikanso, Posakhalitsa anyamata awiri anabwera ndi Bengo aja anayamba kukamba ali uyu kukhala ngati ndi ujayu anakwera Galimoto taisiya kwa Bengo ija eti? Nzake uja mkuzayankha ali aaaaa mmene inatha fuel muja eeee titasika mkuyamba kukankha muja eeeee ndi uyudi munthu uja, koma mmene wathawira titafika pa Roundabout anandiwadza kungoduphira pawindow ngati anaonamo njoka. Apa mbara muja munali phokoso lokhalokha lonseka Ngozo. Guyz KACHASO siwabwinooooo
Posted on: Tue, 05 Aug 2014 11:07:38 +0000

Trending Topics



style="margin-left:0px; min-height:30px;"> They drop out me from the competition of judicial training by the

Recently Viewed Topics




© 2015