KODI IZI NDI ZOONA? BULLETS FC WROTE THIS ON TNM POMPO POMPO - TopicsExpress



          

KODI IZI NDI ZOONA? BULLETS FC WROTE THIS ON TNM POMPO POMPO KUTENGA 3 POINTS: Pa Dziko lonse Lapansi palibenso #LEAGUE yoyendetsedwa mwa chimidzi NDI Mwa umbuli ngati #TNM_SUPERLEAGUE !! Izi sizinachitikepo #Mafco 42 points remaining with 4 games all games to be played at heir Home #chitowe, popanda ya away. #Wanderers 40 points remaining with 4 games 3 away 1 home #Bullets 37 points remaining with 4 games 3 away 1home #Siver 40 points remaining with 4games 3 Home 1 away NB: zachidziwikire kuti Ma Team akumwera sakufunidwa kuti atenge league. ALL The Best #Mafco ntchito akugwilirani kale,Tengani zimenezi. .......@Andy (the undisputed)
Posted on: Mon, 02 Dec 2013 15:52:51 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015