Kwa nonse FB friends,brothers ma Cousy onse ,fellow Poets,amene - TopicsExpress



          

Kwa nonse FB friends,brothers ma Cousy onse ,fellow Poets,amene mudayimila amfumu a Nthiwatiwa,komanso angolomi mchila,akulu akulu azipembedzo,a chipani cholamula cha DPP, komaso sindikuiwala PP, Director wamkulu wa Unkalindanji Moyo DVD bambo Frank Peter Atcheya-Bantu Naligonje ,anzanga akale kale kuyambila ndili mmanja Abiti Anthony Smoke komanso Saul Chipembere ,sindikuyiwa nzanga wamumpesa Gerald Wa Pete ,ulemu kwa nonse amene mudanditumizila mphatso ya cake komanso maluwa ku inbox Ambuye abwezele pamene mwachotsa,ndi enanonse amene mudapeza nthawi pondifunila ine mafuno abwino akubadwa Phwando mukabwele nonse pa 3 August ,2014 ku bwalo la ndakatulo ku Robins Park ,ZIKOMO
Posted on: Sat, 26 Jul 2014 18:40:34 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015