MPHEKESERA ZOMWE ZOLOWA NTAWUNIMU. Pali mphekesera zomwe - TopicsExpress



          

MPHEKESERA ZOMWE ZOLOWA NTAWUNIMU. Pali mphekesera zomwe zikumveka ntawuni, mphekeserayi ikuti akatswiri awiri omwe amasewera team ija ya #SILVER STRIKERS, omwe ndi #LUCKY SAFINTRA MALATA komanso#CHAWANANGWA KAWONGA ayiwuza excutive ya team yi kuti iwo season sakufuna kutimikira team yi koma mmalo mwake aawalole kuti akatumikire team ya fuko ya #BIG BULLETS FC, zifukwa zomwe akatswiri awiriwa apangira ziganizozi komanso munthawi yofanana sizikudziwaka, page ya #BULLETS FC NEWSM SCORES AND LIVE UPDATES MALAWI ikhala ili bisy kuthamangathamanga kuti ipeze zoona zake za nkhaniyi. Tumizani BB ku 1515 kuchokera pa lamya yanu ya mmanja ya tnm . TNM THE OFFICIAL SPONSORS OF MALAWIS ELITE SUPER LEAGUE. #FRAZER
Posted on: Mon, 13 Oct 2014 12:32:44 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015