Malawi the flames has now turn to ashes... chomwe timaziwa - TopicsExpress



          

Malawi the flames has now turn to ashes... chomwe timaziwa ndikusewera bwino ndikulimbikira koma opanda zigoli... vuto limakhala ndi ife ma suporter ndi ma commentetors, we single out some players nkumawati ndima genius ngati amasewera okha team yonseyo ndiye enawo amasowa motivation.. kuyambila goalboy mpaka striker aliyense amatengapo gawo koma timatchukisa ogoletsa yekha. we will remain losers ngati mkhalidwe limeneli lingapitilire.nanga omwe timawatamawo analikuti posagoletsa? tinene kuti u genius wawowo dzulo anauvula kaye? macdonard halawa sangagwire ngati ma defender sakumuteteza bwino, komanso ma defender sangachite bwino ngati pa mid mpila sakuwupanga hold komanso ma strikers sangachite bwino ngati sakulandila mipila yoyenera. so, stop singling out one player to be genius pamalawi pano. 2 -0 ma genius alimmomo? shame on them. genius players!!!!
Posted on: Mon, 08 Sep 2014 03:44:06 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015