Moni mabwana ndi madona? Team ya wanderers yakana kuwalora - TopicsExpress



          

Moni mabwana ndi madona? Team ya wanderers yakana kuwalora anyamata ake awiri CHIPUWA NDI MULIMBIKA kupita ku bullets kotero angofuna maplayer ena anatero mike butao . Sliver striker yati ndiyonkhezeka kupeleka anyamata ake ku bullets chawanangwa ndi malata bullets anatero mcdonald mafuta mwale . Bullets inthakupeza oyinthandiza nthawi ina iliyonse pamene akukasewera caf GS Alord foter watsimikiza zankhaniyi #OMZY.
Posted on: Sun, 28 Dec 2014 07:57:38 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015