Muthandizeni munthuyi Prince Mulomwe , I need help guys..ex - TopicsExpress



          

Muthandizeni munthuyi Prince Mulomwe , I need help guys..ex girl friend wanga akundisowesa mtendere kwabasi.Ndinasi yana naye chifukwa amandidabula ndi azibambo..ulo kudya katundu sindinadyepo olo kamozi amangondipusisa..ndiye nditaona kuti ndachepa nazo ndinangozisiya..I ye sanadandaulenso chifukwa anali ndi amuna ambiri.. Patha zaka 12 chisiyanilane...mwezi watha anandifonera kumandiuza kuti amandikondabe moti akundidikirira kuti ndikazapita ku malawi tizakamange banja..chifukwa panopa ndili RSA...koma akuti ali ndi mwana wa zaka 11..moti last week anapita kwa makolo anga kukaonekera..kodi pamenepa nditani?..ndilibe mkazi panopa koma ndikaganiza chipogwe chomwe amandipanga..sindikumufunanso koma iye wanenesa kuti ndifune olo ndisafune iye ndi mkazi wanga..basi..moti amafona daily..ma sms ndiye osanena..
Posted on: Thu, 31 Oct 2013 15:25:50 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015