Ndinyimbo iti ya oyimba wakumalawi yomwe amakambamo za - TopicsExpress



          

Ndinyimbo iti ya oyimba wakumalawi yomwe amakambamo za xhenophobia? haha atumbuka ndinasiya ku a biffa apa biff ndi nonse muli ku joni ambiri munalonjeza kuti simuzapita ku malawi mpaka bingu azafe kaye pano anamwalira inu simuna bwere hahaha siyaxhoba mzansi!! mubwera ulendo wake ndi uno tiyeni nawo ma comment osonyeza kukwiya pa zomwe ndalembazi....**Themba** wamisala anaona nkhondo kkk...DPP woyee!..UDF woyee..PP woyee!! zipani zonse kumalawi woyeee! anthu ovota akubwera
Posted on: Wed, 17 Jul 2013 19:42:25 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015